aside My first Orgasm…

For fear of butchering the queen’s ranguage as my boss big daddy bae put it recently, I have decided to “wlite” this article in Chichewa, well, mostly Chichewa. It will be “vely” tough for me not to use Engrish but I will try.

“Koma Nayanda, ndiye ukufuna ulembe za orgasm mu Chichewa??” But of course, why not? Why not use my mother tongue to explain my first “pamalungo” experience. Its me, I like to overshare and shock people… stop scrolling down now.

By now you know that I started having sex at seventeen, I told y’all already about how I lost my virginity and stuff but I had my first orgasm when I was twenty three.

I kid you not, nthawi imene ndinkapanga zogonanazo ku college I thought I was doing it all, yes it felt good but I had to experience a real orgasm to know kuti nthawi yonseyi palibe chimene ndimapanga.

Choyamba, nthawi zonse ndikamaliza kuchindana ndi munthu hahahahahahahahahahahahahha…. Eeeeh, mau andivuta kulemba awo… asa… kuchindana…mmm ndinene kuti kunyengana ndi munthu chifukwa ndinazindikira mochedwa kuti zomwe ndimapanga ndikunyengana, kuchindana kumakoma kwambiri, kumakhala kogundika. Okhe, ndinali pati, nthawi zonse ndikamaliza chinyengana ndi munthu ndimamvabe kuyabwa malo ozungulira nyini yanga ngati kuti chinachake chikusowekera.

Ndikakhala kuti timapanga position inayake ndimamva kuti pamene pamayabwa paja pakukandidwa komabe zimapezeka kuti munthu uja sakupafika kwenikweni. Vutonso linali ineyo kuti sindinkadziwa kuti ndichiyani, ndisaname, komabe kunyenganako kumakomabe kwa size yake.

Nde poti ndine munthu okonda kuwerenga zinthu ndikuwonera zinthu ndinayamba kufufuza kuti malo amayabwa aja ndichiyani ndipo ndinaphunzira kuti ndi kananyongo kamene kamayabwa (clitoris). Kwa nthawi yayitali sindinkadziwa kuti kanyembaka kameneka ntchito yake inali chani. Amuna ena akamakaseweresa pena ndinkamva kuwawa, pena kukoma koposa muyezo kuti mpaka ndimalesesa, pena zimangondibhowa chabe m’mene amapangira. Ndinkadabwa kuti amuna amakalimbikira chifukwa chiyani.

Ndiye nditawerenga ntchito yake, ndipo pamene ndinkawelengapo ananenesa kuti ndibwino kuti ndiyesele ndekha. Zinandidzidzimusa kwambiri chifukwa ine ndinali ndisanazigwiregwirepo munjira imeneyo. Ndinazindikira kuti akutanthauza kuti ndibunyule. Ine ndinali olimba mtima kuti ndimvesese kuti kuyabwa komwe ndimamva ndingakuthese bwanji nde ndinapanga chisankho kuti usiku wa tsiku limenelo ndizigwiregwire ndekha.

Zinthu zinayamba kumveka bwinobwino chifukwa mumakanema azogonanawa, ma blue movie, nthawi zambiri atsikana amakonda kuzisewelesa kanyemba kawo kaja nde ndinati aaaah, mwinadi ndizowona.

Usiku utafika, ndinasamba bwinobwino ngati kuti ndikukanyengana ndi mamuna, kuli kuzikomesa ndi kuzikonda ndekhandekha amwene. Ndinaloka chitseko bwinobwino chifukwa pa nthawi imeneyi ndinkakhala ndi makolo… ntheladi, akanati andipezelele nditagundika kusewelesa kanyemba kanga nkanapitisidwa kokapempheleredwa ndithu.Ndinayika tinyimbo tapansipansi, kukhala ngati kuzitotesa ndekha ndithu, kuzipanga ka romansi ndekha.

Ndimayenela kuzipasa nyere ndekha ndithu kuti ndinyowe bwinobwino chifukwa powelenga paja anati kanyembakonso kamayenera kuti kazigwiridwa kali konyowa chifukwa kupanda kutelo, kamawawa. Mpake amuna enawa amatipweteka ndithu, kukagwira kanyemba kali chiumile abale, ngati kuti akupala ndi sand paper, kulakwa mwamva, panyapawo ndithu.

Pang’onopang’ono ka nyerenyere kanayambapo. Ndinazigwiragwira timabele tanga mpakana tinafufuma nato kuti njoooo! Nthawi yonseyo ndinali ndikuganizira mamuna winawake amene anayesesa kundimvesa kukoma kwambiri. Ndikatseka maso ndimaganizira zonse zimene amachita. M’mene amandipsyopsyonela mukhosi mwanga, m’mene amagwirila mabele anga… m’mene mbolo yake imawonekera akatota, ili njooo, misempha, ikupuma, m’mene imamvekera akamalowesa Iiiih ngati kuti moyowu  akuwuzula… ngati kuti mtima wasuntha ulipa nyinipa…

Patapita kanthawi ndinazimva kuti ndikunyowa ndithu. Ndinazigwira pakhomo la nyini, kukowako chikazi chija nkuyamba kuseweletsa kanyemba kanga. Ndinayamba kuzigwira ngati ndikupaka mankhwala pachilonda mozunguliza ndichala chapakati, pang’onopang’ono ndithu. Ndinayamba kumva kukoma ngati kobela chonchi… kathupi kumasuntha ngati monyung’wanyika chonchi. Kenaka ndinayamba kumva kuyabwa ndimamva kuja… kuja ndimamva ndikamaliza kunyengana kuja… ngati ndikusowa mtendere kuti chinachake chikusoweka… osati kusowa mboni iyayi .. . Koma kuti ngati kuti ukudya tchipisi chopanda mchere…

Pamenepo ndiye ndinayamba kusewelesa ndimphamvuko ndithu, mwachanguko, EYA! Koma pamenepo… kumachita kumva kuti apa ndiye ndikumva kukoma, kuti ndikukanda poyabwa paja…. Mayineeeeeee inuyo mukudziwa kupuma nsanga ndikumva kukoma inuyo???? Koma amwene kuzafinya pillow… koma nsanawu kuzapindika, komatu osasiya kusewelesa. Kumafuna kuti ndisiye komanso osafuna kuti ndimalize… komatu sewelesani pamenepaja….

Sindikudziwa kuti ndingafotokoze bwanji zimene ndinayamba kumva pamenepo chifukwa ndiye ndinayamba kuzinyekulira ndekhendekha… kunyekulira ka nyemba. Ndinayamba kupuma mwaphuma, komatu mpaka kutchula dzina lamunthu amene ndimamuganizira uja… koma kumamulilira eti… ngati kuti akundichinda. Inafika nthawi yoti sindingasiyenso iyayi, chala kumakanika kuchoka, komatu kuzaseweresa kwambiri, chilichonse nkuzangoyima, mwinanso ndi nthawi yomwe kuyima…. Thupi nkuzanjejemera, kuzamva kuti nyini ikunjenjemera ngati kuti ikupuma… ma mimbapa kuzanjenjemera, ntchafu kuzanjenjemera, tizalatakuphazi kuzapindika nkuwuma… manja kuwuma.

Akamati  pamalungo ine nkuzamvesa chifukwa nde fever m’mene inayendera pamenepo sindimamvesa. Amayine ndinamva kukoma ine .. . Kuchita kukhumudwa kuti mchindo onse uja ndakhala ndikupanga uja ndinali ndikutaya nthawi ine.. .

Ndinangokhala ngati ndakakamila pabedi, nsana utapindika, nkono utakamila pa bumbu, mtima ukutsika pang’onopan’ono. Ndikati ndigwire kanyemba kaja kamasowesa mtendere kuti sikakuyenera kugwiridwanso… ngati pressure cooker amwene… kuti kaphulika.

Komatu ndinaseka ndekhandekha….

 

I had never felt like that before… that my dear friends, fans and perverts was my first orgasm. Yes it was out of masturbation, zero shame at all. It didn’t even take me five minutes to fall asleep after that explosive feeling. I woke up next morning and did it again and it became kama habit mpaka I got used to it kuti munthu akapanda kundifikiza pamenepopo, ndimamalizisa ndekha.

Pano tinajayira… mpaka kubunyula kosinthira mastyle…

Of course panopa nde I don’t consider it sex unless I have an orgasm like that, in fact every time I have an orgasm… every time… when I don’t munthuyo amauzidwa kuti “man, pamalungo sindinafike” ndipo akapanda kumalizisa, ndimamalizisa ndekha. That feeling is addictive amwene.

From that day on, its safe to say that I stopped kunyengana ndi anthu, tinalowa league yochinda tsopano…aaah, pano ndimachinda… kumaponya mchindo amwene, mukamaliza kumachita kuti, akulu, tachindana eti? Masewela tinasiya. Nkhani ya mchindo iyi osamaphwekesa iyayi… osamaopa malungo iyayi.

Kinda late for 23 years old komabe, ena ali m’ma 40 umu koma zomwe ndafotokoza apa sakudziwa ata!

5 comments

  1. Mpake amuna enawa amatipweteka ndithu, kukagwira kanyemba kali chiumile abale, ngati kuti akupala ndi sand paper, kulakwa mwamva, panyapawo ndithu.

    FAVORITE LINE OF ALL TIME..HAHAHA

    Liked by 1 person

  2. So glad i came accross this! I have been wondering for a while if the word for orgasm (in a female sense) exists in Chichewa or any of our Malawian languages? I fund it sad that in general our chauvinistic society does not recognise that women deserve to enjoy sex as much as men! I am happy you took time to explore your body and found out what makes you tick. No shame in masturbation! Embrace your sexual side 🙂

    Like

Leave a Reply

Fill in your details below or click an icon to log in:

WordPress.com Logo

You are commenting using your WordPress.com account. Log Out /  Change )

Google+ photo

You are commenting using your Google+ account. Log Out /  Change )

Twitter picture

You are commenting using your Twitter account. Log Out /  Change )

Facebook photo

You are commenting using your Facebook account. Log Out /  Change )

Connecting to %s